Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 13:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ndipo kanthu kalikonse koyenera kuwonongedwa* kasamamatire kudzanja lanu,+ kuti mkwiyo woyaka moto wa Yehova usiye kukuyakirani+ ndipo akuchitireni chifundo ndi kukumverani chisoni,+ kutinso akuchulukitseni, monga mmene analumbirira makolo anu.+

  • Salimo 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Kumbukirani chifundo chanu,+ inu Yehova, ndi zochita zanu zosonyeza kukoma mtima kosatha.+

      Pakuti munayamba kuchita zimenezo kale kwambiri.+

  • Salimo 102:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Inu mudzanyamuka ndi kusonyeza Ziyoni chifundo,+

      Pakuti imeneyi ndi nyengo yomukomera mtima,

      Chifukwa nthawi yoikidwiratu yakwana.+

  • Yesaya 54:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “Kwa kanthawi kochepa ndinakusiyiratu,+ koma ndidzakusonkhanitsa pamodzi mwachifundo chachikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena