Salimo 119:126 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 126 Ino ndi nthawi yakuti inu Yehova muchitepo kanthu,+Chifukwa anthu odzikuzawo aphwanya chilamulo chanu.+
126 Ino ndi nthawi yakuti inu Yehova muchitepo kanthu,+Chifukwa anthu odzikuzawo aphwanya chilamulo chanu.+