Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 9:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Nyamukani, inu Yehova! Munthu asakuposeni mphamvu.+

      Anthu a mitundu ina aweruzidwe pamaso panu.+

  • Salimo 102:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Inu mudzanyamuka ndi kusonyeza Ziyoni chifundo,+

      Pakuti imeneyi ndi nyengo yomukomera mtima,

      Chifukwa nthawi yoikidwiratu yakwana.+

  • Yesaya 28:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Yehova adzaimirira monga mmene anachitira paphiri la Perazimu.+ Adzakalipa ngati mmene anachitira m’chigwa cha kufupi ndi Gibeoni+ kuti achite ntchito yake. Ntchito yakeyo ndi yodabwitsa. Adzakalipa kuti achite zochita zake. Zochita zakezo n’zachilendo.+

  • Yeremiya 18:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma inu Yehova mukudziwa bwino chiwembu chimene andikonzera kuti andiphe.+ Musakhululukire* cholakwa chawo, ndipo musafafanize tchimo lawolo pamaso panu. Koma iwo apunthwe pamaso panu.+ Muwachitire zimenezi pa nthawi ya mkwiyo wanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena