Salimo 119:129 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 129 Zikumbutso zanu n’zodabwitsa.+N’chifukwa chake ine ndimazisunga.+