Salimo 119:143 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 143 Zowawa ndi zovuta zinandigwera.+Koma ndinakonda malamulo anu.+