Salimo 119:149 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 149 Imvani mawu anga mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Inu Yehova, ndisungenibe wamoyo mogwirizana ndi zigamulo zanu.+
149 Imvani mawu anga mwa kukoma mtima kwanu kosatha.+Inu Yehova, ndisungenibe wamoyo mogwirizana ndi zigamulo zanu.+