Salimo 119:152 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 152 Zina mwa zikumbutso zanu ndinazidziwa kale kwambiri,+Pakuti munazikhazikitsa kalekale.+