Salimo 119:144 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 144 Zikumbutso zanu zidzakhalabe zolungama mpaka kalekale.+Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti ndikhalebe ndi moyo.+ Mlaliki 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndazindikira kuti zonse zimene Mulungu woona amapanga zimakhala mpaka kalekale.+ Palibe choti n’kuwonjezerapo kapena choti n’kuchotsapo.+ Mulungu woona ndi amene wapanga zimenezi,+ kuti anthu azimuopa.+
144 Zikumbutso zanu zidzakhalabe zolungama mpaka kalekale.+Ndithandizeni kukhala wozindikira kuti ndikhalebe ndi moyo.+
14 Ndazindikira kuti zonse zimene Mulungu woona amapanga zimakhala mpaka kalekale.+ Palibe choti n’kuwonjezerapo kapena choti n’kuchotsapo.+ Mulungu woona ndi amene wapanga zimenezi,+ kuti anthu azimuopa.+