Salimo 132:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adani ake ndidzawaveka manyazi,+Koma ufumu*+ wake udzapita patsogolo.”+