Salimo 135:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wochita zimenezi ndiye anapha ana oyamba kubadwa a ku Iguputo,+Anapha ana a anthu ngakhalenso ana a nyama.+
8 Wochita zimenezi ndiye anapha ana oyamba kubadwa a ku Iguputo,+Anapha ana a anthu ngakhalenso ana a nyama.+