Salimo 136:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yamikani amene anapha mafumu amphamvu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
17 Yamikani amene anapha mafumu amphamvu:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+