Salimo 136:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yamikani Mulungu wakumwamba:+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+