Miyambo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:1 Nsanja ya Olonda,7/15/2001, tsa. 24
10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+