Miyambo 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mthenga woipa amayambitsa mavuto,+ koma nthumwi yokhulupirika imachiritsa.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:17 Nsanja ya Olonda,7/15/2004, ptsa. 28-29