Miyambo 25:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nkhani yabwino yochokera kudziko lakutali+ ili ngati madzi ozizira kwa munthu wotopa.+ 2 Akorinto 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero ndife+ akazembe+ m’malo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife.+ Monga okhala m’malo mwa Khristu tikupempha kuti:+ “Gwirizananinso ndi Mulungu.” 2 Timoteyo 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Zinthu zimene unazimva kwa ine ndi kwa mboni zambiri+ zokhudza ine, zimenezo uziphunzitse kwa anthu okhulupirika amene nawonso, adzakhala oyenerera bwino kuphunzitsa ena.+
20 Chotero ndife+ akazembe+ m’malo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife.+ Monga okhala m’malo mwa Khristu tikupempha kuti:+ “Gwirizananinso ndi Mulungu.”
2 Zinthu zimene unazimva kwa ine ndi kwa mboni zambiri+ zokhudza ine, zimenezo uziphunzitse kwa anthu okhulupirika amene nawonso, adzakhala oyenerera bwino kuphunzitsa ena.+