Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 15:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Maso+ owala amapangitsa mtima kusangalala.+ Uthenga+ wabwino umanenepetsa mafupa.+

  • Yesaya 52:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Mapazi+ a munthu yemwe akuyenda pamwamba pa mapiri pobweretsa uthenga wabwino, ndi okongola kwabasi!+ Munthu yemwe akulengeza za mtendere,+ yemwe akubweretsa uthenga wabwino wa zinthu zabwino kuposa kale,+ yemwe akulengeza za chipulumutso,+ yemwe akuuza Ziyoni kuti: “Mulungu wako wakhala mfumu.”+

  • Luka 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma mngeloyo anawauza kuti: “Musaope! Ine ndabwera kudzalengeza kwa inu uthenga wabwino wa chimwemwe chachikulu chimene anthu onse adzakhala nacho.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena