Rute 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maso ako akhale pamunda umene akukolola, ndipo uzipita nawo limodzi kumeneko. Anyamatawa ndawalamula kuti asakukhudze.+ Ukamva ludzu, nawenso uzipita kumitsuko kukamwa madzi amene anyamatawa azitunga.”+ 2 Samueli 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Patapita nthawi, Davide anafotokoza zimene anali kulakalaka kuti: “Ndikanakonda ndikanamwa madzi a m’chitsime cha ku Betelehemu chimene chili pachipata!”+ Mateyu 10:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha m’kapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pang’ono.”+
9 Maso ako akhale pamunda umene akukolola, ndipo uzipita nawo limodzi kumeneko. Anyamatawa ndawalamula kuti asakukhudze.+ Ukamva ludzu, nawenso uzipita kumitsuko kukamwa madzi amene anyamatawa azitunga.”+
15 Patapita nthawi, Davide anafotokoza zimene anali kulakalaka kuti: “Ndikanakonda ndikanamwa madzi a m’chitsime cha ku Betelehemu chimene chili pachipata!”+
42 Aliyense wopatsa mmodzi wa tiana iti ngakhale madzi ozizira okha m’kapu kuti amwe chifukwa ndi wophunzira, ndithu ndikukuuzani, ameneyo mphoto yake sidzatayika ngakhale pang’ono.”+