Miyambo 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amakondwera ndi uchitsiru,+ koma munthu wozindikira ndi amene amayenda panjira yabwino.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:21 Nsanja ya Olonda,8/1/2006, tsa. 183/15/1997, ptsa. 14-15
21 Munthu wopanda nzeru mumtima mwake amakondwera ndi uchitsiru,+ koma munthu wozindikira ndi amene amayenda panjira yabwino.+