Miyambo 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera, amakhala ngati ndolo* yagolide, ndiponso ngati chokongoletsera chagolide wapadera.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 25:12 Nsanja ya Olonda,12/15/1997, tsa. 32
12 Munthu wanzeru akamadzudzula munthu wa khutu lomvetsera, amakhala ngati ndolo* yagolide, ndiponso ngati chokongoletsera chagolide wapadera.+