Miyambo 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zilonda zovulazidwa ndi munthu wokukonda zimakhala zokhulupirika,+ koma kuti munthu wodana nawe akupsompsone pamafunika kumuchonderera.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 27:6 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 183 Nsanja ya Olonda,12/1/2000, tsa. 219/15/1990, tsa. 28
6 Zilonda zovulazidwa ndi munthu wokukonda zimakhala zokhulupirika,+ koma kuti munthu wodana nawe akupsompsone pamafunika kumuchonderera.+