Mlaliki 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati munthu atabereka ana 100+ n’kukhala ndi moyo zaka zambirimbiri, masiku a moyo wake n’kukhala ochuluka,+ koma moyo wake osakhutira ndi zinthu zabwino,+ komanso osalowa m’manda,+ ndithu mwana amene anabadwa wakufa ali bwino kuposa iyeyu.+
3 Ngati munthu atabereka ana 100+ n’kukhala ndi moyo zaka zambirimbiri, masiku a moyo wake n’kukhala ochuluka,+ koma moyo wake osakhutira ndi zinthu zabwino,+ komanso osalowa m’manda,+ ndithu mwana amene anabadwa wakufa ali bwino kuposa iyeyu.+