Mlaliki 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale munthu atakhala ndi moyo zaka 2,000, koma sanasangalale ndi zabwino,+ kodi phindu lake n’chiyani? Pajatu aliyense amapita kumalo amodzi.+
6 Ngakhale munthu atakhala ndi moyo zaka 2,000, koma sanasangalale ndi zabwino,+ kodi phindu lake n’chiyani? Pajatu aliyense amapita kumalo amodzi.+