Mlaliki 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama amagwirira pakamwa pawo,+ koma moyo wawo sukhuta.