Mlaliki 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Dziko iwe, kodi zidzakuthera bwanji ngati mfumu yako ili kamnyamata,+ ndipo akalonga ako amangokhalira kudya ngakhale m’mawa?
16 Dziko iwe, kodi zidzakuthera bwanji ngati mfumu yako ili kamnyamata,+ ndipo akalonga ako amangokhalira kudya ngakhale m’mawa?