Nyimbo ya Solomo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Onsewo atenga malupanga ndipo ndi ophunzitsidwa nkhondo. Aliyense wamangirira lupanga lake m’chiuno mwake kuti adziteteze ku zoopsa za usiku.”+
8 Onsewo atenga malupanga ndipo ndi ophunzitsidwa nkhondo. Aliyense wamangirira lupanga lake m’chiuno mwake kuti adziteteze ku zoopsa za usiku.”+