Nyimbo ya Solomo 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Inu ana aakazi a Ziyoni, pitani panja mukaone Mfumu Solomo itavala nkhata yamaluwa,+ imene mayi ake+ anailukira pa tsiku la ukwati wake, pa tsiku limene mtima wa mfumuyo unasangalala.”+
11 “Inu ana aakazi a Ziyoni, pitani panja mukaone Mfumu Solomo itavala nkhata yamaluwa,+ imene mayi ake+ anailukira pa tsiku la ukwati wake, pa tsiku limene mtima wa mfumuyo unasangalala.”+