Nyimbo ya Solomo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wachikondi wanga atachotsa dzanja lake pabowo la chitseko, m’mimba mwanga+ munabwadamuka.