Nyimbo ya Solomo 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Alonda+ amene anali kuyendayenda mumzinda anandipeza. Anandimenya, anandivulaza. Alonda a pamipanda+ anandilanda chofunda changa.
7 Alonda+ amene anali kuyendayenda mumzinda anandipeza. Anandimenya, anandivulaza. Alonda a pamipanda+ anandilanda chofunda changa.