-
Nyimbo ya Solomo 5:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Mutu wake ndi wokongola ngati golide, golide woyengedwa bwino. Tsitsi lake lili ngati zipatso za kanjedza. Tsitsi lakelo ndi lakuda ngati khwangwala.
-