Nyimbo ya Solomo 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndinati, ‘Ndikwera mtengo wa kanjedza kuti ndikathyole nthambi zake zokhala ndi zipatso.’+ Mabere ako akhale ngati zipatso za mpesa, ndipo mpweya wa m’kamwa mwako ununkhire ngati maapozi.
8 Ine ndinati, ‘Ndikwera mtengo wa kanjedza kuti ndikathyole nthambi zake zokhala ndi zipatso.’+ Mabere ako akhale ngati zipatso za mpesa, ndipo mpweya wa m’kamwa mwako ununkhire ngati maapozi.