Yesaya 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Taonani! Mzinda wokhulupirika uja+ wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+ ndipo zachilungamo zinali kukhala mwa iye,+ koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:21 Yesaya 1, ptsa. 29-31
21 Taonani! Mzinda wokhulupirika uja+ wasanduka hule.+ Unali wodzaza ndi chilungamo+ ndipo zachilungamo zinali kukhala mwa iye,+ koma tsopano muli zigawenga zopha anthu.+