Yesaya 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pakuti anthu adzachita manyazi ndi mitengo ikuluikulu imene inu munali kuilakalaka,+ ndipo mudzagwetsa nkhope zanu chifukwa cha minda imene mwasankha.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:29 Yesaya 1, ptsa. 34-35 Nsanja ya Olonda,10/15/1987, tsa. 12
29 Pakuti anthu adzachita manyazi ndi mitengo ikuluikulu imene inu munali kuilakalaka,+ ndipo mudzagwetsa nkhope zanu chifukwa cha minda imene mwasankha.+