Yesaya 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti ilo ndi tsiku la Yehova wa makamu.+ Tsikulo lidzafikira aliyense wodzitukumula ndi wodzikweza. Lidzafikiranso aliyense wokwezeka kapena wotsika.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:12 Yesaya 1, ptsa. 51-53, 56
12 Pakuti ilo ndi tsiku la Yehova wa makamu.+ Tsikulo lidzafikira aliyense wodzitukumula ndi wodzikweza. Lidzafikiranso aliyense wokwezeka kapena wotsika.+