Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Fuulani, anthu inu,+ chifukwa tsiku la Yehova lili pafupi.+ Lidzabwera ngati kuti Wamphamvuyonse akulanda zinthu.+

  • Yeremiya 46:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Limeneli ndi tsiku la Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa ndipo ndi tsiku lobwezera chilango kwa adani ake.+ Lupanga lidzadya adaniwo ndi kukhuta ndipo lidzamwa magazi awo kufikira litathetsa ludzu lake. Lidzatero pakuti Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ ali ndi nsembe imene akufuna kupereka+ m’dziko la kumpoto, m’mphepete mwa mtsinje wa Firate.+

  • Ezekieli 13:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Amuna inu, simudzapita kukakhala m’mipata ya mpanda+ kuti mukamenye nkhondo, kapena kuti mukamangire nyumba ya Isiraeli mpanda wamiyala+ n’cholinga chakuti mudzadziteteze pa nkhondo ya m’tsiku la Yehova.”+

  • Amosi 5:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+

  • 1 Atesalonika 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti inu eni mukudziwa bwino kuti tsiku la Yehova*+ lidzabwera ndendende ngati mbala usiku.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena