Yesaya 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndi mauta awo, adzaphwanyaphwanya ngakhale anyamata awo.+ Iwo sadzamvera chisoni zipatso za m’mimba.+ Diso lawo silidzamvera chisoni ana aamuna. Yeremiya 50:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, m’dzikomo simudzakhalanso anthu+ ndipo dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayang’ana modabwa ndi kumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+
18 Ndi mauta awo, adzaphwanyaphwanya ngakhale anyamata awo.+ Iwo sadzamvera chisoni zipatso za m’mimba.+ Diso lawo silidzamvera chisoni ana aamuna.
13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, m’dzikomo simudzakhalanso anthu+ ndipo dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayang’ana modabwa ndi kumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+