Yesaya 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu azidzalamulirana mwankhanza, ndipo munthu azidzachitira nkhanza munthu mnzake.+ Mnyamata adzaukira nkhalamba,+ ndipo wonyozeka adzaukira wolemekezeka.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:5 Yesaya 1, ptsa. 56-57
5 Anthu azidzalamulirana mwankhanza, ndipo munthu azidzachitira nkhanza munthu mnzake.+ Mnyamata adzaukira nkhalamba,+ ndipo wonyozeka adzaukira wolemekezeka.+