Yesaya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno kunyumba ya Davide kunapita uthenga wakuti: “Dziko la Siriya layamba kudalira dziko la Efuraimu.”+ Choncho mtima wa Ahazi ndi wa anthu ake unayamba kunjenjemera, ngati mmene mitengo ya m’nkhalango imagwederera ndi mphepo.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:2 Yesaya 1, tsa. 102
2 Ndiyeno kunyumba ya Davide kunapita uthenga wakuti: “Dziko la Siriya layamba kudalira dziko la Efuraimu.”+ Choncho mtima wa Ahazi ndi wa anthu ake unayamba kunjenjemera, ngati mmene mitengo ya m’nkhalango imagwederera ndi mphepo.+