Yesaya 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mutu wa Efuraimu ndiwo Samariya,+ ndipo mutu wa Samariya ndiwo mwana wa Remaliya.+ Anthu inu mukakhala opanda chikhulupiriro, simukhalitsa.”’”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:9 Yesaya 1, tsa. 106
9 Mutu wa Efuraimu ndiwo Samariya,+ ndipo mutu wa Samariya ndiwo mwana wa Remaliya.+ Anthu inu mukakhala opanda chikhulupiriro, simukhalitsa.”’”+