Yesaya 8:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Popeza anthu awa akana+ madzi a ku Silowa+ amene amayenda pang’onopang’ono, ndipo atengeka+ ndi Rezini ndiponso mwana wa Remaliya,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:6 Yesaya 1, ptsa. 113-114
6 “Popeza anthu awa akana+ madzi a ku Silowa+ amene amayenda pang’onopang’ono, ndipo atengeka+ ndi Rezini ndiponso mwana wa Remaliya,+