Salimo 36:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inu ndinu kasupe wa moyo.+Chifukwa cha kuwala kochokera kwa inu, tikuona kuwala.+ Yeremiya 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Inu Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli,+ onse amene akukusiyani adzachita manyazi.+ Mayina a anthu onse okupandukirani+ adzalembedwa pafumbi chifukwa asiya Yehova magwero a madzi amoyo.+ Yohane 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anamuuza kuti: “Pita ukasambe+ m’dziwe la Siloamu”+ (dzina limene kumasulira kwake ndi ‘Otumidwa’). Choncho anapita kukasamba,+ ndipo anabwerako akuona.+
13 Inu Yehova, chiyembekezo cha Isiraeli,+ onse amene akukusiyani adzachita manyazi.+ Mayina a anthu onse okupandukirani+ adzalembedwa pafumbi chifukwa asiya Yehova magwero a madzi amoyo.+
7 Kenako anamuuza kuti: “Pita ukasambe+ m’dziwe la Siloamu”+ (dzina limene kumasulira kwake ndi ‘Otumidwa’). Choncho anapita kukasamba,+ ndipo anabwerako akuona.+