Yesaya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova akuwabweretsera+ Mtsinje*+ wa madzi ambiri ndi amphamvu, womwe ndi mfumu ya Asuri+ ndi ulemerero wake wonse.+ Iyo idzadzaza timitsinje take tonse n’kusefukira mpaka m’mphepete mwa mitsinje yake yonse, Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:7 Yesaya 1, ptsa. 113-114
7 Yehova akuwabweretsera+ Mtsinje*+ wa madzi ambiri ndi amphamvu, womwe ndi mfumu ya Asuri+ ndi ulemerero wake wonse.+ Iyo idzadzaza timitsinje take tonse n’kusefukira mpaka m’mphepete mwa mitsinje yake yonse,