Yesaya 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa makamu, dzikolo layaka moto ndipo anthu adzakhala ngati chakudya cha motowo.+ Palibe amene adzamvere chisoni aliyense, ngakhale m’bale wake.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:19 Yesaya 1, ptsa. 139-140
19 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova wa makamu, dzikolo layaka moto ndipo anthu adzakhala ngati chakudya cha motowo.+ Palibe amene adzamvere chisoni aliyense, ngakhale m’bale wake.+