Yesaya 14:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzathyola Msuri amene ali m’dziko langa+ ndipo ndidzamupondaponda pamapiri anga.+ Goli lake lidzachoka pa iwo ndipo katundu wake adzachoka pamapewa awo.”+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:25 Yesaya 1, tsa. 189
25 Ndidzathyola Msuri amene ali m’dziko langa+ ndipo ndidzamupondaponda pamapiri anga.+ Goli lake lidzachoka pa iwo ndipo katundu wake adzachoka pamapewa awo.”+