Yesaya 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Hesiboni ndi Eleyale+ akulira mofuula. Mawu awo amveka mpaka ku Yahazi.+ N’chifukwa chake amuna onyamula zida a ku Mowabu akungofuula. Mitima yawo ikuchita mantha kwambiri.
4 Hesiboni ndi Eleyale+ akulira mofuula. Mawu awo amveka mpaka ku Yahazi.+ N’chifukwa chake amuna onyamula zida a ku Mowabu akungofuula. Mitima yawo ikuchita mantha kwambiri.