Yesaya 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero Mowabu adzalira mofuula chifukwa cha tsoka lake. Aliyense wokhala m’Mowabu ndithu adzalira mofuula.+ Omenyedwawo adzalirira mphesa zouma zoumba pamodzi za ku Kiri-hareseti,+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:7 Yesaya 1, tsa. 193
7 Chotero Mowabu adzalira mofuula chifukwa cha tsoka lake. Aliyense wokhala m’Mowabu ndithu adzalira mofuula.+ Omenyedwawo adzalirira mphesa zouma zoumba pamodzi za ku Kiri-hareseti,+