Yesaya 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni.+ Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha Nebo+ ndi Medeba.+ Anthu onse a mmenemo ameta mipala.+ Ndevu za munthu aliyense zametedwa. Yeremiya 48:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Anthu a ku Mowabu achita manyazi pakuti agwidwa ndi mantha aakulu.+ Lirani mofuula. Amuna inu, lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wafunkhidwa.
2 Iye wapita kukachisi ndi ku Diboni.+ Wapita kumalo okwezeka kukalira. Mowabu akulira mofuula chifukwa cha Nebo+ ndi Medeba.+ Anthu onse a mmenemo ameta mipala.+ Ndevu za munthu aliyense zametedwa.
20 Anthu a ku Mowabu achita manyazi pakuti agwidwa ndi mantha aakulu.+ Lirani mofuula. Amuna inu, lengezani ku Arinoni+ kuti Mowabu wafunkhidwa.