Yesaya 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimenezi zidzakhala chizindikiro ndi umboni kwa Yehova wa makamu m’dziko la Iguputo,+ pakuti iwo adzalirira Yehova chifukwa cha anthu owapondereza,+ ndipo iye adzawatumizira mpulumutsi wamkulu amene adzawapulumutse.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:20 Nsanja ya Olonda,1/1/2000, ptsa. 9-10 Yesaya 1, tsa. 205
20 Zimenezi zidzakhala chizindikiro ndi umboni kwa Yehova wa makamu m’dziko la Iguputo,+ pakuti iwo adzalirira Yehova chifukwa cha anthu owapondereza,+ ndipo iye adzawatumizira mpulumutsi wamkulu amene adzawapulumutse.+