Luka 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa lero wakubadwirani Mpulumutsi,+ amene ndi Khristu Ambuye,+ mumzinda wa Davide.+