Yesaya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+ Yesaya 19:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zimenezi zidzakhala chizindikiro ndi umboni kwa Yehova wa makamu m’dziko la Iguputo,+ pakuti iwo adzalirira Yehova chifukwa cha anthu owapondereza,+ ndipo iye adzawatumizira mpulumutsi wamkulu amene adzawapulumutse.+
6 Pakuti kwa ife kwabadwa mwana.+ Ife tapatsidwa mwana wamwamuna,+ ndipo paphewa pake padzakhala ulamuliro.+ Iye adzapatsidwa dzina lakuti Mlangizi Wodabwitsa,+ Mulungu Wamphamvu,+ Atate Wosatha,+ Kalonga Wamtendere.+
20 Zimenezi zidzakhala chizindikiro ndi umboni kwa Yehova wa makamu m’dziko la Iguputo,+ pakuti iwo adzalirira Yehova chifukwa cha anthu owapondereza,+ ndipo iye adzawatumizira mpulumutsi wamkulu amene adzawapulumutse.+