-
Yesaya 23:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kodi uwu ndi mzinda wanu uja, umene unali wosangalala kuyambira kalekale, kuyambira pa chiyambi pake? Mapazi ake anali kuutengera kutali kuti ukakhale ngati mlendo.
-